smallholder tea poster12sep

Ndondomeko zofunikira za ulimi oyenera
- Za alimi ang'onoang'ono a tiyi Kuteteza mbewu ku tizilombo (kuthana ndi matenda
wotchedwa Armilaria owononga mitengo ya tiyi)

Mtengo wa tiyi wang'aluka
ndipo ukutulutsa tiufa toyera

Zulani phata lonse ndi mizu
yomwe ndipo mutenthe

Kuteteza mbewu ku tizilombo (kutengulira)

Kasamalidwe ka zinyalala zomwe zimatha kuwola

Kupanga manyowa kuchokela ku
zinyalala zomwe zimatha kuwola

Kuwotcha zinyalala

Kusamala madzi oyipa pakhomo


Madzi
Kutengulira tiyi kuti tizilombo tisapitilire
kufala. Nthambi zomwe zadulidwa zitha
kugwiritsidwa ntchito pophimbira mbewu.

Tizilombo tikupitilira
kuwononga tiyi

Zipangizo zozitetezela

Kupopela osaziteteza

Chovala kunkhope chotchinjiliza
kuti mankhwala asakukhudzeni

Chovala choteteza
ku mvula

Kupopela ndi zozitetezela


Kasungidwe ka mankhwala

Kutaya madzi mu nkhuti momwe
mwabzalidwa nthochi (Dziwani izi: ngati
madzi akupanga zithaphwi (sakuyenda),
mukumbe dzenje ndikuikamo miyala)

Kutaya madzi oyipa
kutsogolo kwa nyumba

Kutsuka zipangizo

Kutsuka zipangizo mu
mtsinje kapena dziwe

Kutaya madzi ochapila
mu dimba lomwe
lathilidwa mankhwala

Kapena, kutaya madzi

mu nkhuti yomwe muli
makala

Kusamala chilengedwe

Bulugama
Mtsinje ukuwuma

Kusunga mankhwala
m'nyumba

Mwachitsanzo, khola lankhuku
lakale mutha kulisandutsa
mosungira mankhwala.
Ikanimo pulasitiki mkati

M'golo wa
chitsulo mutha
kuusandutsa
mosungira


Kasamalidwe ka zinyalala za pulasitiki ndi mabotolo
Potolela
a mankhwala
Mabotolo
opanda

Mabotolo opanda kanthu
komanso zinyalala za pulasitiki
zatayidwa pansi
Version: June 2011

zinyalala za
pulasitiki

mabotolo a
mankhwala ndi
zinyalala za
pulasitiki,
onetsetsani kuti

mwazisiyanitsa
(pamapeto pa
zonse,
otsogolera gulu
watolela zonse)

Bulugama amaumitsa
mitsinje ndi zitsime

Kuzula bulugama
amene ali pafupi
ndi mtsinje

Mtsinje wabwelera
mchimake

Kuteteza nthaka kuti
isakokoloke

Vuto la kukokoloka kwa

nthaka

Kubzala mitengo yachilengedwe ndi nsenjere
kuti muteteze nthaka komanso madzi